Home Menu Files Zatsopano Mode
Thu, 21 Nov 2024 18:11:38 +0000

ZOKHUNZA HALFLONG

Halflong ndi chani?

Kadulidwe ka halflong

Zofunika podula halflong

Logtable ya halflong

HALF LONG

Halflong ndi thupi limene limakhala ku mtunda kwa dress.Back to top

KADULIDWE KA HALF LONG

Tikamadula halflong timayamba ndi kupanga samu ya pa CHEST (C), (formula yake ndi: (C+3 or 5) /4 + 1.5 or 1) Timapinda nsalu potengera yankho lomwe tapeza ndipo tikamaipinda, timaichotsa kumanja n'kumaipititsa kumanzere. Tikatero tiyeze nsalu yathu yapamwambayo ndi samu ija ya pa chest.Back to top

ZOFUNIKA PODULA HALFLONG

Tiyenera kuyeza kutalika kwa Halflong pa nsalu yopindidwayo. Timayeza kuchokera pansi kupita m'mwamba mwa halflong komanso kuchoka kumtunda kupita m'musi. Poyeza timagwiritsa ntchito formula iyi: 1/2L + 1

Kadulidwe ka halflong

1. KUTAMBALALA KWA KHOSI

  • Mwana: 2 or 2.25
  • Medium: 2.5, 2.75, 3, 3.5
  • Mkulu: 3, 3.5, 4, 4.5
  • Mbali za halflong

    Ngat munthu ali ndi chest cha 33 ndie kuti tiphatikiza 3 ndi kugawa ndi 4 nkuzaphatikiza 1 yomwe ndi 10.

  • kutambalala kwa khosi ndi 3
  • kuya kwa khosi koyamba=2
  • kuya kwa khosi kwachiwiri=3.5
  • khwapa mwa "J" shape=8
  • 2. KUYA KWA KHOSI KOYAMBA

  • Wamkulu: 2, 2.5, 3.5, 4
  • Mwana: 1.25, 1.5
  • Wa medium: 1.75, 2, 2.5, 3
  • 3. KUYA KWA KHOSI KACHIWIRI

    Timangochosera kuya kwa khosi koyamba ku 5.5 kenako timayeza

    4. Kuyeza kaba C/2

    5. Kuseseresa phewa

    6. Kudula mzere wa nsalu yowonjezera m'mbali 1.5

    7. Kujambula khwapa J shape

    8. Kujambula bevulo yoyamba pa nsalu yathu yapansi.

    >Back to top Chimwemwe.wapkiz.com Ifeyo.wapkiz.com